Eksodo 35:18 - Buku Lopatulika18 zichiri za chihema, ndi zichiri za kubwalo, ndi zingwe zao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 zichiri za chihema, ndi zichiri za kubwalo, ndi zingwe zao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 zikhomo zake pamodzi ndi zingwe za chihema cha Chauta ndi za bwalo lake; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 zikhomo za tenti ya chihema ndiponso za bwalo, ndi zingwe zake; Onani mutuwo |