Eksodo 35:14 - Buku Lopatulika14 ndi choikaponyali cha kuunika, ndi zipangizo zake, ndi nyali zake, ndi mafuta a kuunika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 ndi choikapo nyali cha kuunika, ndi zipangizo zake, ndi nyali zake, ndi mafuta a kuunika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 choikaponyale ndi zipangizo zake, nyale zake ndi mafuta a nyalezo; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 choyikapo nyale yowunikira pamodzi ndi zipangizo zake, nyale ndi mafuta anyalezo; Onani mutuwo |