Eksodo 29:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo utero nao Aroni, ndi ana ake aamuna, monga mwa zonse ndakuuza; udzaze manja ao masiku asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo utero nao Aroni, ndi ana ake amuna, monga mwa zonse ndakuuza; udzaze manja ao masiku asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 “Zonse zimene ndakulamulazi umchitire Aroni ndi ana ake aamuna omwe. Udzachite mwambo wakuŵapatula pa masiku asanu ndi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 “Uchitire Aaroni ndi ana ake aamuna zonse zimene ndakulamulazi. Uchite mwambo wowapatula kukhala ansembe masiku asanu ndi awiri. Onani mutuwo |