Chivumbulutso 9:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anali nazo zikopa ngati zikopa zachitsulo; ndipo mkokomo wa mapiko ao ngati mkokomo wa agaleta, a akavalo ambiri akuthamangira kunkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anali nazo zikopa ngati zikopa zachitsulo; ndipo mkokomo wa mapiko ao ngati mkokomo wa agaleta, a akavalo ambiri akuthamangira kunkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pachifuwa pake panali mamba onga ngati malaya achitsulo apachifuwa. Kulira kwa mapiko ake kunali ngati kwa magareta ankhondo ambiri okokedwa ndi akavalo othamangira ku nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Dzombelo linavala za pachifuwa zachitsulo. Phokoso la mapiko awo linali ngati phokoso la magaleta ankhondo ambiri okokedwa ndi akavalo othamangira ku nkhondo. Onani mutuwo |