Chivumbulutso 8:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo angelo asanu ndi awiri akukhala nao malipenga anadzikonzera kuti aombe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo angelo asanu ndi awiri akukhala nao malipenga anadzikonzera kuti aombe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono angelo asanu ndi aŵiri amene anali ndi malipenga asanu ndi aŵiri aja adakonzeka kuti alize malipengawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Angelo asanu ndi awiri anakonzekera kuyimba malipenga asanu ndi awiri. Onani mutuwo |