Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Chivumbulutso 7:7 - Buku Lopatulika

7 Mwa fuko la Simeoni zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko Levi zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Isakara zikwi khumi ndi ziwiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Mwa fuko la Simeoni zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko Levi zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Isakara zikwi khumi ndi ziwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 A m'fuko la Simeoni anali zikwi khumi ndi ziŵiri. A m'fuko la Levi anali zikwi khumi ndi ziŵiri. A m'fuko la Isakara anali zikwi khumi ndi ziŵiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 ochokera fuko la Simeoni analipo 12,000; ochokera fuko la Levi analipo 12,000; ochokera fuko la Isakara analipo 12,000;

Onani mutuwo Koperani




Chivumbulutso 7:7
14 Mawu Ofanana  

Ndipo anatenganso pakati nabala mwana wamwamuna, nati, Tsopano lino mwamuna wanga adzadziphatika kwa ine chifukwa ndambalira iye ana aamuna atatu; chifukwa chake anamutcha dzina lake Levi.


Ndipo Leya anati, Mulungu wandipatsa ine mphotho yanga, chifukwa ndapatsa mdzakazi wanga kwa mwamuna wanga: namutcha dzina lake Isakara.


ana aamuna a Leya: ndiwo Rubeni mwana woyamba wa Yakobo, ndi Simeoni ndi Levi, ndi Yuda, ndi Zebuloni, ndi Isakara;


Adamanga mwana wa kavalo wake pampesa, ndi mwana wa bulu wake pa mpesa wosankhika; natsuka malaya ake m'vinyo, ndi chofunda chake m'mwazi wa mphesa.


Simeoni ndi Levi ndiwo abale; zida za mphulupulu ndizo malupanga ao.


Ndipo maina a ana aamuna a Levi, mwa kubadwa kwao ndiwo: Geresoni, ndi Kohati, ndi Merari; ndipo zaka za moyo wa Levi ndizo zana limodzi mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri.


A ana a Simeoni, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, owerengedwa ao, powerenga maina mmodzimmodzi, amuna onse kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Koma dzina la Mwisraele adamuphayo, ndiye amene adamupha pamodzi ndi mkazi Mmidiyani, ndiye Zimiri mwana wa Salu, mfumu ya nyumba ya makolo mwa Asimeoni.


Iwo ndiwo mabanja a Asimeoni, zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana ziwiri.


Ndipo maere achiwiri anamtulukira Simeoni, fuko la ana a Simeoni monga mwa mabanja ao; ndi cholowa chao chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.


Maere achinai anamtulukira Isakara, kunena za ana a Isakara monga mwa mabanja ao.


Mwa fuko la Asere zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Nafutali zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Manase zikwi khumi ndi ziwiri.


Mwa fuko la Zebuloni zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Yosefe zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Benjamini anasindikizidwa chizindikiro zikwi khumi ndi ziwiri.


Ndipo Yuda ananena ndi Simeoni mkulu wake, Kwera nane ku gawo langa kuti tiwathire nkhondo Akanani; ndipo inenso ndidzamuka nawe ku gawo lako. Namuka naye Simeoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa