Chivumbulutso 7:6 - Buku Lopatulika6 Mwa fuko la Asere zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Nafutali zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Manase zikwi khumi ndi ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mwa fuko la Asere zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Nafutali zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Manase zikwi khumi ndi ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 A m'fuko la Asere anali zikwi khumi ndi ziŵiri. A m'fuko la Nafutali anali zikwi khumi ndi ziŵiri. A m'fuko la Manase anali zikwi khumi ndi ziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 ochokera fuko la Aseri analipo 12,000; ochokera fuko la Nafutali analipo 12,000; ochokera fuko la Manase analipo 12,000; Onani mutuwo |