Chivumbulutso 5:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anadza, nalitenga kudzanja lamanja la Iye wakukhala pa mpando wachifumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anadza, nalitenga kudzanja lamanja la Iye wakukhala pa mpando wachifumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Iyeyo adabwera nkulandira buku lija limene linali m'dzanja lamanja la wokhala pampando wachifumu uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye anabwera natenga buku lija limene linali mʼdzanja lamanja la wokhala pa mpando waufumuyo. Onani mutuwo |