Chivumbulutso 5:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo ndinalira kwambiri, chifukwa sanapezeke mmodzi woyenera kutsegula bukulo, kapena kulipenya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo ndinalira kwambiri, chifukwa sanapezedwa mmodzi woyenera kutsegula bukulo, kapena kulipenya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Motero ndidalira kwambiri poona kuti sadapezeke woyenera kufutukula bukulo kapena kuyang'anamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndinalira kwambiri chifukwa panalibe amene anapezeka woyenera kufutukula bukuli kapena kuona zamʼkati mwake. Onani mutuwo |