Chivumbulutso 5:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo sanathe mmodzi mu Mwamba, kapena padziko, kapena pansi padziko kutsegula pabukupo, kapena kulipenya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo sanathe mmodzi m'Mwamba, kapena padziko, kapena pansi pa dziko kutsegula pabukupo, kapena kulipenya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma panalibe ndi mmodzi yemwe Kumwamba, kapena pa dziko lapansi, kapena kunsi kwa dziko, wotha kufutukula bukulo kapena kuyang'anamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma panalibe ndi mmodzi yemwe kumwamba kapena pa dziko lapansi kapena kunsi kwa dziko lapansi woti afutukule bukulo kapena kuona zamʼkati mwake. Onani mutuwo |