Chivumbulutso 5:10 - Buku Lopatulika10 ndipo mudawayesa iwo ufumu ndi ansembe kwa Mulungu wathu; ndipo achita ufumu padziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndipo mudawayesa iwo ufumu ndi ansembe kwa Mulungu wathu; ndipo achita ufumu padziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mudaŵasandutsa mtundu wachifumu ndi ansembe otumikira Mulungu wathu, ndipo adzakhala olamulira pa dziko lapansi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Inu munawasandutsa kukhala mtundu waufumu ndi ansembe otumikira Mulungu, ndipo adzalamulira dziko lapansi.” Onani mutuwo |
Ndipo ndinaona mipando yachifumu, ndipo anakhala pamenepo; ndipo anawapatsa chiweruziro; ndipo ndinaona mizimu ya iwo amene adawadula khosi chifukwa cha umboni wa Yesu, ndi chifukwa cha mau a Mulungu, ndi iwo amene sanalambire chilombo, kapena fano lake, nisanalandire lembalo pamphumi ndi padzanja lao; ndipo anakhala ndi moyo, nachita ufumu pamodzi ndi Khristu zaka chikwi.