Chivumbulutso 2:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Smirina lemba: Izi anena woyamba ndi wotsiriza, amene anakhala wakufa, nakhalanso ndi moyo: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Smirina lemba: Izi anena woyamba ndi wotsiriza, amene anakhala wakufa, nakhalanso ndi moyo: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Mtsogoleri wa mpingo wa ku Smirina umlembere kuti: Naŵa mau ochokera kwa Iye amene ali Woyamba ndiponso Wotsiriza, amene adaafa nkukhalanso moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Lembera mngelo wa mpingo wa ku Simurna kuti: Awa ndi mawu ochokera kwa amene ndi Woyamba ndi Wotsiriza, amene anafa nʼkukhalanso ndi moyo. Onani mutuwo |