Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Chivumbulutso 2:6 - Buku Lopatulika

6 Koma ichi uli nacho, kuti udana nazo ntchito za Anikolai, zimene Inenso ndidana nazo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Koma ichi uli nacho, kuti udana nazo ntchito za Anikolai, zimene Inenso ndidana nazo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Komabe chokomera chanu ndi ichi chakuti, mumadana ndi zochita za Anikolai, zimene inenso ndimadana nazo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Komabe chokomera chako ndi chakuti umadana ndi zochita za Anikolai, zimene Inenso ndimadana nazo.

Onani mutuwo Koperani




Chivumbulutso 2:6
7 Mawu Ofanana  

Natuluka Yehu mwana wa Hanani mlauli kukomana naye, nati kwa mfumu Yehosafati, Muyenera kodi kuthandiza zoipa, ndi kukonda amene adana ndi Yehova? Chifukwa cha ichi ukugwerani mkwiyo wochokera kwa Yehova.


Sindidzaika chinthu choipa pamaso panga; chochita iwo akupatuka padera chindiipira; sichidzandimamatira.


Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa.


Iye wokhala nalo khutu amve chimene Mzimu anena kwa Mipingo. Kwa iye amene apambana ndidzampatsa kudya za ku mtengo wa moyo umene uli mu Paradaiso wa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa