Chivumbulutso 18:1 - Buku Lopatulika1 Zitatha izi ndinaona mngelo wina wakutsika mu Mwamba wakukhala nao ulamuliro waukulu; ndipo dziko linaunikidwa ndi ulemerero wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Zitatha izi ndinaona mngelo wina wakutsika m'Mwamba wakukhala nao ulamuliro waukulu; ndipo dziko linaunikidwa ndi ulemerero wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Zitatha izi, ndidaona mngelo wina akutsika kuchokera Kumwamba. Anali ndi ulamuliro waukulu, ndipo pa dziko lonse lapansi padayera chifukwa cha kuŵala kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Zitatha izi ndinaona mngelo wina akutsika kuchokera kumwamba. Iye anali ndi ulamuliro waukulu, ndipo dziko lapansi linawala ndi ulemerero. Onani mutuwo |