Chivumbulutso 16:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo wachitatu anatsanulira mbale yake kumitsinje ndi akasupe a madzi; ndipo kunasanduka mwazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo wachitatu anatsanulira mbale yake kumitsinje ndi akasupe a madzi; ndipo kunasanduka mwazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kenaka mngelo wachitatu adakhuthulira za mumkhate mwake pa mitsinje, ndi pa akasupe a madzi. Pomwepo madziwo adasanduka magazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mngelo wachitatu anapita natsanula mbale yake pa mitsinje ndi akasupe amadzi ndipo zinasanduka magazi. Onani mutuwo |
Chifukwa chanji ndinafika osapeza munthu? Ndi kuitana koma panalibe wina woyankha? Kodi dzanja langa lafupika konse, kuti silingathe kuombola? Pena Ine kodi ndilibe mphamvu zakupulumutsa? Taona pa kudzudzula kwanga ndiumitsa nyanja, ndi kusandutsa mitsinje chipululu; nsomba zake zinunkha chifukwa mulibe madzi, ndipo zifa ndi ludzu.