Chivumbulutso 11:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo a mwa anthu ndi mafuko, ndi manenedwe, ndi mitundu apenyera mitembo yao masiku atatu ndi nusu lake, osalola mitembo yao iikidwe m'manda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo a mwa anthu ndi mafuko, ndi manenedwe, ndi mitundu apenyera mitembo yao masiku atatu ndi nusu lake, osalola mitembo yao iikidwe m'manda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Anthu a mitundu yonse, a mafuko onse ndiponso a zilankhulo zonse azidzayang'anitsitsa mitemboyo masiku atatu ndi hafu, akukana kuti iikidwe m'manda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kwa masiku atatu ndi theka, anthu ochokera ku mtundu uliwonse, fuko lililonse, chiyankhulo chilichonse ndi dziko lililonse, azidzayangʼanitsitsa mitembo yawoyo koma adzakana kuyikwirira. Onani mutuwo |