Chivumbulutso 10:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo mau ndinawamva ochokera Kumwamba, analankhulanso nane, nanena, Muka, tenga buku lofunyululalo m'dzanja la mngelo wakuimirira panyanja ndi padziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo mau ndinawamva ochokera Kumwamba, analankhulanso nane, nanena, Muka, tenga buku lofunyululalo m'dzanja la mngelo wakuimirira panyanja ndi padziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamenepo mau amene ndidaamva kuchokera Kumwamba adandilankhulanso, adati, “Pita, katenge kampukutu kofutukula kaja kamene kali m'manja mwa mngelo woponda pa nyanja ndi pa mtunda uja.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pamenepo mawu amene ndinamva kuchokera kumwamba aja, anandiyankhulanso, anati, “Pita katenge buku lotsekulidwalo mʼdzanja la mngelo amene waponda pa nyanja ndi pa mtundayo.” Onani mutuwo |