Chivumbulutso 10:2 - Buku Lopatulika2 ndipo anali nako m'dzanja lake kabuku kofunyulula: ndipo anaponda nalo phazi lake lamanja panyanja, ndi lamanzerelo pamtunda, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndipo anali nako m'dzanja lake kabuku kofunyulula: ndipo anaponda nalo phazi lake lamanja panyanja, ndi lamanzerelo pamtunda, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 M'manja mwake anali ndi kampukutu kofutukula. Ndi mwendo wa ku dzanja lamanja adaaponda pa nyanja, ndi wakumanzere adaaponda pa mtunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mʼdzanja lake munali kabuku kakangʼono kotsekulidwa. Phazi lake lamanja linaponda mʼnyanja ndipo phazi lake lamanzere linaponda pa mtunda. Onani mutuwo |