Chivumbulutso 1:10 - Buku Lopatulika10 Ndinagwidwa ndi Mzimu tsiku la Ambuye, ndipo ndinamva kumbuyo kwanga mau aakulu, ngati a lipenga, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndinagwidwa ndi Mzimu tsiku la Ambuye, ndipo ndinamva kumbuyo kwanga mau akulu, ngati a lipenga, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pa tsiku la Ambuye ndidaagwidwa ndi Mzimu Woyera, nkumva kumbuyo kwanga liwu lamphamvu ngati kulira kwa lipenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pa tsiku la Ambuye ndinanyamulidwa ndi Mzimu ndipo ndinamva kumbuyo kwanga mawu ofuwula ngati lipenga, Onani mutuwo |