Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Amosi 5:24 - Buku Lopatulika

24 Koma chiweruzo chiyende ngati madzi, ndi chilungamo ngati mtsinje wosefuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Koma chiweruzo chiyende ngati madzi, ndi chilungamo ngati mtsinje wosefuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Koma kuweruza kwanu kwangwiro kuziyenda kosalekeza ngati madzi, kulungama kwanu kukhale ngati mtsinje wosaphwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Koma chiweruzo cholungama chiyende ngati madzi, chilungamo ngati mtsinje wosaphwa!

Onani mutuwo Koperani




Amosi 5:24
11 Mawu Ofanana  

Kuchita chilungamo ndi chiweruzo kupambana ndi nsembe kumkonda Yehova.


Mwenzi utamvera malamulo anga mtendere wako ukanakhala ngati mtsinje, ndi chilungamo chako monga mafunde a nyanja;


Yehova atero: Chitani chiweruzo ndi chilungamo, landitsani ofunkhidwa m'dzanja la wosautsa; musachite choipa, musamchitire mlendo chiwawa, kapena ana amasiye, kapena akazi amasiye, musakhetse mwazi wosachimwa pamalo pano.


Atero Ambuye Yehova, Likufikireni akalonga a Israele inu, lekani kuchita chiwawa, ndi kulanda za eni ake; muchite chiweruzo ndi chilungamo; lekani kupirikitsa anthu anga m'zolowa zao, ati Ambuye Yehova.


Pakuti ndikondwera nacho chifundo, si nsembe ai; ndi kumdziwa Mulungu kuposa nsembe zopsereza.


Mundichotsere phokoso la nyimbo zanu; sindifuna kumva mayimbidwe a zisakasa zanu.


inu osintha chiweruzo chikhale chivumulo, nimugwetsa pansi chilungamo.


Iye anakuuza, munthuwe, chomwe chili chokoma; ndipo Yehova afunanji nawe koma kuti uchite cholungama, ndi kukonda chifundo ndi kuyenda modzichepetsa ndi Mulungu wako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa