Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Amosi 5:23 - Buku Lopatulika

23 Mundichotsere phokoso la nyimbo zanu; sindifuna kumva mayimbidwe a zisakasa zanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Mundichotsere phokoso la nyimbo zanu; sindifuna kumva mayimbidwe a zisakasa zanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Musandisokose nazo nyimbo zanu zachipembedzo, sindingathe kupirira kulira kwa azeze anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Musandisokose nazo nyimbo zanu! Sindidzamvetsera kulira kwa azeze anu.

Onani mutuwo Koperani




Amosi 5:23
5 Mawu Ofanana  

Inde, mungakhale mupereka kwa Ine nsembe zanu zopsereza, ndi nsembe zaufa, sindidzazilandira Ine; ndi nsembe zoyamika za ng'ombe zanu zonenepa, sindidzazisamalira Ine.


Koma chiweruzo chiyende ngati madzi, ndi chilungamo ngati mtsinje wosefuka.


akungoimba kutsata maliridwe a zeze, nadzilingiririra zoimbira nazo ngati Davide;


Ndipo ndidzasanduliza zikondwerero zanu zikhale maliro, ndi nyimbo zanu zikhale za maliro, ndi kufikitsa ziguduli m'chuuno monse, ndi mpala pamutu uliwonse; nadzakhala ngati maliro a mwana mmodzi yekha, ndi chitsiriziro chake ngati tsiku lowawa.


Koma nyimbo za ku Kachisi zidzasanduka kubuma tsiku ilo, ati Ambuye Yehova; mitembo idzachuluka; adzaitaya paliponse padzakhala zii.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa