Amosi 5:10 - Buku Lopatulika10 Iwo adana naye wodzudzula kuchipata, nanyansidwa naye wolunjikitsa mau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Iwo adana naye wodzudzula kuchipata, nanyansidwa naye wolunjikitsa mau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Inu mumadana ndi muweruzi wodzudzula zosalungama, mumanyansidwa ndi wokamba zoona pa bwalo lamilandu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 inu mumadana ndi amene amadzudzula mʼbwalo la milandu ndi kunyoza amene amanena zoona. Onani mutuwo |