Amosi 1:15 - Buku Lopatulika15 ndipo mfumu yao idzalowa kundende, iyo ndi akalonga ake pamodzi, ati Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 ndipo mfumu yao idzalowa kundende, iyo ndi akalonga ake pamodzi, ati Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsono mfumu yao idzatengedwa kunka ku ukapolo, iyoyo pamodzi ndi nduna zake.” Akuterotu Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mfumu yawo idzatengedwa kupita ku ukapolo, iyo pamodzi ndi akuluakulu ake,” akutero Yehova. Onani mutuwo |