Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ahebri 6:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo potero atapirira analandira lonjezanolo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo potero atapirira analandira lonjezanolo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Nchifukwa chake Abrahamu adaayembekeza molimbikira, nalandira zimene Mulungu adaamlonjeza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Ndipo Abrahamu atayembekezera mofatsa, analandira zimene anamulonjezazo.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 6:15
10 Mawu Ofanana  

Ndipo anamuka Abramu monga Yehova ananena kwa iye, ndipo Loti anamuka pamodzi naye: ndipo Abramu anali wa zaka makumi asanu ndi awiri kudza zisanu, pamene anatuluka mu Harani.


Ana a Israele ndipo anaswana, nabalana, nachuluka, nakhala nazo mphamvu zazikulu; ndipo dziko linadzala nao.


kuti musakhale aulesi, koma akuwatsanza iwo amene alikulowa malonjezano mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima.


Ndipo mwa ichi ali Nkhoswe ya chipangano chatsopano, kotero kuti, popeza kudachitika imfa yakuombola zolakwa za pa chipangano choyamba, oitanidwawo akalandire lonjezano la zolowa zosatha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa