Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 13:19 - Buku Lopatulika

19 Ndipo ndikudandaulirani koposa kuchita ichi, kuti kubwera kwanga kwa inu kufulumidwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Ndipo ndikudandaulirani koposa kuchita ichi, kuti kubwera kwanga kwa inu kufulumidwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Ndikukupemphani makamaka kuti mupemphere kuti Mulungu andibwezere kwa inu msanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Ine ndikukupemphani kuti mundipempherere kuti Mulungu andibwezere kwa inu msanga.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 13:19
4 Mawu Ofanana  

Koma undikonzerenso pogona; pakuti ndiyembekeza kuti mwa mapemphero anu ndidzapatsidwa kwa inu.


Koma ndidandaulira inu, abale, lolani mau a chidandauliro; pakutinso ndalembera inu mwachidule.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa