Ahebri 12:21 - Buku Lopatulika21 ndipo maonekedwewo anali oopsa otere, kuti Mose anati, Ndiopatu ndi kunthunthumira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 ndipo maonekedwewo anali oopsa otere, kuti Mose anati, Ndiopatu ndi kunthunthumira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Maonekedwe a zonsezo anali oopsa kwambiri, kotero kuti Mose yemwe adaati, “Ndikunjenjemera ndi mantha.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Maonekedwenso a Mose anali woopsa kwambiri, ngakhale Mose yemwe anati, “Ine ndinachita mantha ndi kunjenjemera.” Onani mutuwo |