Ahebri 12:20 - Buku Lopatulika20 pakuti sanakhoze kulola cholamulidwacho. Ingakhale nyama ikakhudza phirilo, idzaponyedwa miyala; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 pakuti sanakhoza kulola cholamulidwacho. Ingakhale nyama ikakhudza phirilo, idzaponyedwa miyala; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 pakuti lidaaŵaopsa lamulo lija lakuti, “Ndi nyama yomwe ikangokhudza phirilo, iphedwe ndi miyala.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Iwo anachita mantha ndi lamulo lija lakuti, “Ngakhale nyama ikangokhudza phirilo, iphedwe ndi miyala.” Onani mutuwo |