Ahebri 11:35 - Buku Lopatulika35 Akazi analandira akufa ao mwa kuuka kwa akufa; ndipo ena anakwapulidwa, osalola kuomboledwa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Akazi analandira akufa ao mwa kuuka kwa akufa; ndipo ena anakwapulidwa, osalola kuomboledwa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Akazi ena adalandiranso anthu ao amene adafa, ataŵaukitsa. Ena adazunzidwa koopsa mpaka kufa, osalola kuti aŵamasule, chifukwa chofuna kudzaukanso ndi moyo wabwino kopambana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Amayi ena analandira anthu awo amene anafa, ataukitsidwanso. Enanso anazunzidwa ndipo anakana kumasulidwa, kuti adzaukenso ndi moyo wabwino. Onani mutuwo |