Ahebri 11:31 - Buku Lopatulika31 Ndi chikhulupiriro Rahabu wadama uja sanaonongeke pamodzi ndi osamverawo, popeza analandira ozonda ndi mtendere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndi chikhulupiriro Rahabu wadama uja sanaonongeka pamodzi ndi osamverawo, popeza analandira ozonda ndi mtendere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Pokhala ndi chikhulupiriro, Rahabu, mkazi wadama uja, sadafe nawo limodzi anthu osamvera aja, pakuti adaaŵalandira bwino azondi aja kunyumba kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Ndi chikhulupiriro Rahabe, mkazi wadama sanaphedwe pamodzi ndi osamvera aja chifukwa analandira bwino ozonda aja ku nyumba kwake. Onani mutuwo |