Ahebri 11:30 - Buku Lopatulika30 Ndi chikhulupiriro malinga a Yeriko adagwa atazunguliridwa masiku asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndi chikhulupiriro malinga a Yeriko adagwa atazunguliridwa masiku asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Pokhala ndi chikhulupiriro, malinga a mzinda wa Yeriko adagwa, Aisraele ataŵazungulira masiku asanu ndi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndi chikhulupiriro mpanda wa Yeriko unagwa, Aisraeli atawuzungulira kasanu ndi kawiri. Onani mutuwo |