Ahebri 11:28 - Buku Lopatulika28 Ndi chikhulupiriro anachita Paska, ndi kuwaza kwa mwazi, kuti wakuononga ana oyamba angawakhudze iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndi chikhulupiriro anachita Paska, ndi kuwaza kwa mwazi, kuti wakuononga ana oyamba angawakhudze iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Pokhala ndi chikhulupiriro, adachita nawo chikondwerero cha Paska, nalamula kuti anthu awaze magazi pa zitseko kuti mngelo woononga ana achisamba uja asakhudze ana achisamba a Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Ndi chikhulupiriro anachita Paska ndi kuwaza magazi, kuti mngelo wowononga ana oyamba kubadwa asaphe ana oyamba kubadwa a Aisraeli. Onani mutuwo |