Ahebri 11:24 - Buku Lopatulika24 Ndi chikhulupiriro Mose, atakula msinkhu, anakana kutchedwa mwana wake wa mwana wamkazi wa Farao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndi chikhulupiriro Mose, atakula msinkhu, anakana kutchedwa mwana wake wa mwana wamkazi wa Farao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Pokhala ndi chikhulupiriro, Mose atakula adakana kutchedwa mdzukulu wa Farao, mfumu ya ku Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ndi chikhulupiriro Mose atakula, anakana kutchedwa mwana wa mwana wamkazi wa Farao. Onani mutuwo |