Ahebri 11:15 - Buku Lopatulika15 Ndipotu akadakumbukira lijalo adatulukamo akadaona njira yakubwerera nayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipotu akadakumbukira lijalo adatulukamo akadaona njira yakubwera nayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Akadakhala kuti ankaganizirako za kudziko kumene adaachokera, bwenzi atapeza danga lakuti abwerere kwakaleko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Akanakhala kuti akuganizira za dziko limene analisiya akanapeza mpata obwerera kwawo. Onani mutuwo |