Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ahebri 10:37 - Buku Lopatulika

37 Pakuti katsala kanthawi kakang'onong'ono, ndipo wakudzayo adzafika, wosachedwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Pakuti katsala kanthawi kakang'onong'ono, ndipo wakudzayo adzafika, wosachedwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Paja Malembo akuti, “Pangotsala kanthaŵi pang'ono chabe kuti Iye amene alikudza, afike. Sachedwa ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Pakuti nʼkanthawi kochepa chabe, Iye amene akubwera adzabwera ndipo sadzachedwa ayi.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 10:37
11 Mawu Ofanana  

Idzani, anthu anga, lowani m'zipinda mwanu, nimutseke pamakomo panu; nimubisale kanthawi kufikira mkwiyo utapita.


Wamng'ono adzasanduka chikwi, ndi wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu; Ine Yehova ndidzafulumiza ichi m'nthawi yake.


nati kwa Iye, Inu ndinu wakudza kodi, kapena tiyembekezere wina?


Ndinena ndi inu, adzawachitira chilungamo posachedwa. Koma Mwana wa Munthu pakudza Iye, adzapeza chikhulupiriro padziko lapansi kodi?


Kufatsa kwanu kuzindikirike ndi anthu onse. Ambuye ali pafupi.


osaleka kusonkhana kwathu pamodzi, monga amachita ena, komatu tidandaulirane, ndiko koposa monga momwe muona tsiku lilikuyandika.


Koma ichi chimodzi musaiwale, okondedwa inu, kuti tsiku limodzi likhala kwa Ambuye ngati zaka chikwi, ndi zaka chikwi ngati tsiku limodzi.


Ambuye sazengereza nalo lonjezano, monga ena achiyesa chizengerezo; komatu aleza mtima kwa inu, wosafuna kuti ena aonongeke, koma kuti onse afike kukulapa.


Iye wakuchitira umboni izi, anena, Indetu; ndidza msanga. Amen; idzani, Ambuye Yesu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa