Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Aefeso 5:24 - Buku Lopatulika

24 Komatu monga Mpingo amvera Khristu, koteronso akazi amvere amuna ao m'zinthu zonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Komatu monga Mpingo amvera Khristu, koteronso akazi amvere amuna ao m'zinthu zonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Tsono monga Mpingo umamvera Khristu, momwemonso akazi azimvera amuna ao pa zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Tsono monga mpingo umagonjera Khristu, momwemonso akazi akuyenera kugonjera amuna awo mu zonse.

Onani mutuwo Koperani




Aefeso 5:24
10 Mawu Ofanana  

Ndipo samalirani zonse ndanena ndi inu; nimusatchule dzina la milungu ina; lisamveke pakamwa pako.


Ndipo utero nao Aroni, ndi ana ake aamuna, monga mwa zonse ndakuuza; udzaze manja ao masiku asanu ndi awiri.


Ndipo makumi asanu ndi awiri aja anabwera mokondwera, nanena, Ambuye, zingakhale ziwanda zinatigonjera ife m'dzina lanu.


Pakuti mwamuna ndiye mutu wa mkazi, monganso Khristu ndiye mutu wa Mpingo, ali yekha Mpulumutsi wa thupilo.


Amuna inu, kondani akazi anu, monganso Khristu anakonda Mpingo, nadzipereka yekha m'malo mwake;


Komanso inu, yense pa yekha, yense akonde mkazi wake wa iye yekha, monga adzikonda yekha; ndipo mkaziyo akumbukire kuti aziopa mwamuna.


Ana inu, mverani akubala inu m'zonse, pakuti ichi Ambuye akondwera nacho.


Akapolo inu, mverani m'zonse iwo amene ali ambuye monga mwa thupi, wosati ukapolo wa pamaso, monga okondweretsa anthu, komatu ndi mtima wakulinga kumodzi, akuopa Ambuye;


m'zonse udzionetsere wekha chitsanzo cha ntchito zabwino; m'chiphunzitso chako uonetsere chosavunda, ulemekezeko,


Akapolo amvere ambuye ao a iwo okha, nawakondweretse m'zonse; osakana mau ao;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa