Aefeso 4:24 - Buku Lopatulika24 nimuvale munthu watsopano, amene analengedwa monga mwa Mulungu, m'chilungamo, ndi m'chiyero cha choonadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 nimuvale munthu watsopano, amene analengedwa monga mwa Mulungu, m'chilungamo, ndi m'chiyero cha choonadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Ndipo muvale moyo watsopano, umene Mulungu adaulenga, wofanafana naye. Apo mudzakhala olungama ndi oyera mtima kwenikweni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 ndi kuti muvale umunthu watsopano, wolengedwa kuti ufanane ndi Mulungu mu chilungamo chenicheni ndi chiyero. Onani mutuwo |