Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Timoteyo 4:21 - Buku Lopatulika

21 Tayesetsa kudza isanadze nyengo yachisanu. Akukupatsa moni Yubulo, ndi Pude, ndi Lino, ndi Klaudia, ndi abale onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Tayesetsa kudza isanadze nyengo yachisanu. Akukupatsa moni Yubulo, ndi Pude, ndi Lino, ndi Klaudia, ndi abale onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Uyesetse ndithu kubwera isanafike nyengo yachisanu. Yubulo, Pude, Lino, Klaudia, ndi abale ena onse akuti moni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Uyesetse kubwera kuno nthawi yozizira isanafike. Eubulo akupereka moni, ndiponso Pude, Lino, Klaudiya ndi abale onse nawonso akupereka moni.

Onani mutuwo Koperani




2 Timoteyo 4:21
11 Mawu Ofanana  

Pakuti pamene ulikupita naye mnzako wa mlandu kwa oweruza, fulumira panjira kutha naye mlandu, kuti angakokere iwe kwa oweruza, ndipo oweruzayo angapereke iwe kwa msilikali, ndi msilikali angaponye iwe m'nyumba yandende.


Akupatsani moni abale onse. Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika.


Oyera mtima onse akupatsani moni.


Oyera mtima onse akupatsani inu moni, koma makamaka iwo a banja la Kaisara.


pokhumba usiku ndi usana kukuona iwe, ndi kukumbukira misozi yako, kuti ndidzazidwe nacho chimwemwe;


Chofunda chija ndinachisiya ku Troasi kwa Karpo, udze nacho pakudza iwe, ndi mabuku, makamaka zikopa zija zolembedwa.


Tayesetsa kudza kwa ine msanga:


Pamene ndikatuma Aritema kwa iwe, kapena Tikiko, chita changu kudza kwa ine ku Nikopoli: pakuti ndatsimikiza mtima kugonerako nyengo yachisanu.


Akupereka moni ana a mbale wanu wosankhika.


koma ndiyembekeza kukuona iwe msanga, ndipo tidzalankhula popenyana.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa