2 Timoteyo 4:13 - Buku Lopatulika13 Chofunda chija ndinachisiya ku Troasi kwa Karpo, udze nacho pakudza iwe, ndi mabuku, makamaka zikopa zija zolembedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Chofunda chija ndinachisiya ku Troasi kwa Karpo, udze nacho pakudza iwe, ndi mabuku, makamaka zikopa zija zolembedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Pobwera unditengereko mwinjiro wanga umene ndidasiya kwa Karpo ku Troasi. Unditengerenso mabuku anga, makamaka aja azikopaŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pobwera, unditengere chofunda pamwamba chimene ndinachisiya kwa Kupro ku Trowa. Unditengerenso mabuku anga, makamaka aja azikopawa. Onani mutuwo |