Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Timoteyo 3:7 - Buku Lopatulika

7 ophunzira nthawi zonse, koma sangathe konse kufikira kuchizindikiritso cha choonadi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 ophunzira nthawi zonse, koma sakhoza konse kufikira kuchizindikiritso cha choonadi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 amangomvera za aliyense, ndipo sangathe konse kudziŵa choona.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 amaphunzira nthawi zonse koma samatha kuzindikira choonadi.

Onani mutuwo Koperani




2 Timoteyo 3:7
14 Mawu Ofanana  

Wonyoza afunafuna nzeru osaipeza; koma wozindikira saona vuto m'kuphunzira.


Ndipo Iye anayankha nati, Chifukwa kwapatsidwa kwa inu kudziwa zinsinsi za Ufumu wa Kumwamba, koma sikunapatsidwe kwa iwo.


Mungathe inu bwanji kukhulupirira, popeza mulandira ulemu wina kwa mnzake ndipo ulemu wakuchokera kwa Mulungu yekha simuufuna?


Kuti tisakhalenso makanda, ogwedezekagwedezeka, natengekatengeka ndi mphepo yonse ya chiphunzitso, ndi tsenga la anthu, ndi kuchenjerera kukatsata chinyengo cha kusocheretsa;


koma Yehova sanakupatseni mtima wakudziwa, ndi maso akupenya, ndi makutu akumva, kufikira lero lino.


amene afuna anthu onse apulumuke, nafike pozindikira choonadi.


wolangiza iwo akutsutsana mofatsa; ngati kapena Mulungu awapatse iwo chitembenuziro, kukazindikira choonadi,


Za iye tili nao mau ambiri kuwanena, ndi otivuta powatanthauzira, popeza mwagontha m'makutu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa