Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Timoteyo 2:23 - Buku Lopatulika

23 Koma mafunso opusa ndi opanda malango upewe, podziwa kuti abala ndeu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Koma mafunso opusa ndi opanda malango upewe, podziwa kuti abala ndeu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Uzikana matsutsano opusa ndi opanda nzeru, paja ukudziŵa kuti zotere zimautsa mikangano.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Ukane matsutsano oyipa ndi opusa, chifukwa amayambitsa mikangano.

Onani mutuwo Koperani




2 Timoteyo 2:23
7 Mawu Ofanana  

kapena asasamale nkhani zachabe, ndi mawerengedwe osalekeza a mafuko a makolo, ndiwo akuutsa mafunso, osati za udindo wa Mulungu umene uli m'chikhulupiriro;


koma nkhani zachabe ndi za akazi okalamba ukane. Ndipo udzizoloweretse kuchita chipembedzo;


Uwakumbutse izi, ndi kuwachitira umboni pamaso pa Ambuye, kuti asachite makani ndi mau osapindulitsa kanthu, koma ogwetsa iwo akumva.


Koma pewa nkhani zopanda pake; pakuti adzapitirira kutsata chisapembedzo,


koma pewa mafunso opusa, ndi mawerengedwe a mibadwo, ndi ndeu, ndi makani a pamalamulo; pakuti sizipindulitsa, ndipo zili zachabe.


Zichokera kuti nkhondo, zichokera kuti zolimbana mwa inu? Kodi sizichokera kuzikhumbitso zanu zochita nkhondo m'ziwalo zanu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa