2 Timoteyo 1:17 - Buku Lopatulika17 komatu pokhala mu Roma iye anandifunafuna ine ndi khama, nandipeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 komatu pokhala m'Roma iye anandifunafuna ine ndi khama, nandipeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 adangoti atafika ku Roma, nkuyamba kundifunafuna mwachangu, mpaka adandipeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mʼmalo mwake, atangofika ku Roma, anandifunafuna ndipo anandipeza. Onani mutuwo |