Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Timoteyo 1:11 - Buku Lopatulika

11 umene ndaikikapo mlaliki, ndi mtumwi ndi mphunzitsi wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 umene ndaikikapo mlaliki, ndi mtumwi ndi mphunzitsi wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Mulungu adandiika kuti ndikhale mlaliki, mtumwi ndi mphunzitsi wa Uthenga Wabwino umenewu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ine ndinasankhidwa kukhala wamthenga, ndi mtumwi ndi mphunzitsi wa Uthenga Wabwinowu.

Onani mutuwo Koperani




2 Timoteyo 1:11
5 Mawu Ofanana  

Koma Ambuye anati kwa iye, Pita; pakuti iye ndiye chotengera changa chosankhika, chakunyamula dzina langa pamaso pa amitundu ndi mafumu ndi ana a Israele;


Kodi sindine mfulu? Kodi sindine mtumwi? Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu? Kodi simuli inu ntchito yanga mwa Ambuye?


pofuna kukhala aphunzitsi a malamulo ngakhale sadziwitsa zimene azinena, kapena azilimbikirazi.


umene anandiika ine mlaliki wake ndi mtumwi (ndinena zoona, wosanama ine), mphunzitsi wa amitundu m'chikhulupiriro ndi choonadi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa