Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Petro 3:6 - Buku Lopatulika

6 mwa izi dziko lapansi la masiku aja, pomizika ndi madzi, lidaonongeka;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 mwa izi dziko lapansi la masiku aja, pomizika ndi madzi, lidaonongeka;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndipo ndi madzi okhaokhawo dziko lapansi la masiku amenewo lidamizidwa ndi kuwonongedwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Ndi madzinso achigumula, dziko lapansi la masiku amenewo linawonongedwa.

Onani mutuwo Koperani




2 Petro 3:6
6 Mawu Ofanana  

ndipo ndidzakumbukira pangano langa limene lili ndi Ine ndi inu, ndi zamoyo zonse zokhala ndi moyo; ndipo madzi sadzakhalanso konse chigumula chakuononga zamoyo zonse.


Taona atsekera madzi, naphwa; awatsegulira, ndipo akokolola dziko lapansi.


Anadya, anamwa, anakwatira, anakwatiwa, kufikira tsiku lija Nowa analowa m'chingalawa, ndipo chinadza chigumula, nkuwaononga onsewo.


ndipo sanalekerere dziko lapansi lakale, koma anasunga Nowa mlaliki wa chilungamo, ndi anzake asanu ndi awiri, pakulitengera dziko la osapembedza chigumula;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa