2 Mbiri 9:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anati kwa mfumu, Inali yoona mbiri ija ndidaimva m'dziko langa, ya machitidwe anu, ndi ya nzeru zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anati kwa mfumu, Inali yoona mbiri ija ndidaimva m'dziko langa, ya machitidwe anu, ndi ya nzeru zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamenepo idauza mfumu Solomoni kuti, “Zimene ndinkamva ndili kudziko la kwathu zonena za ntchito zanu ndi nzeru zanu, nzoonadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iyo inati kwa mfumu, “Mbiri imene ndinamva ndili ku dziko kwathu, ya zomwe munachita komanso nzeru zanu ndi yoona. Onani mutuwo |