2 Mbiri 9:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo mfumu yaikazi ya ku Sheba ataiona nzeru ya Solomoni, ndi nyumba adaimanga, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo mfumu yaikazi ya ku Sheba ataiona nzeru ya Solomoni, ndi nyumba adaimanga, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono itaona nzeru zonse za Solomoni, nyumba imene adaamanga ija, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mfumu yayikazi ya ku Seba itaona nzeru za Solomoni komanso nyumba yaufumu imene anamanga, Onani mutuwo |