2 Mbiri 9:10 - Buku Lopatulika10 Ndiponso anyamata a Huramu, ndi anyamata a Solomoni otenga golide ku Ofiri, anatenga mitengo yambawa ndi timiyala ta mtengo wapatali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndiponso anyamata a Huramu, ndi anyamata a Solomoni otenga golide ku Ofiri, anatenga mitengo yambawa ndi timiyala ta mtengo wapatali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Komanso anyamata a mfumu Hiramu pamodzi ndi anyamata a Solomoni amene adaabwera ndi golide wa ku Ofiri, adabweranso ndi mitengo ya mbawa ndi miyala yamtengowapatali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 (Anthu a Hiramu ndi anthu a Solomoni anabweretsa golide kuchokera ku Ofiri ndipo anabweretsanso mitengo ya mʼbawa ndi miyala yokongola. Onani mutuwo |