2 Mbiri 8:9 - Buku Lopatulika9 Koma mwa ana a Israele Solomoni sanawayese akapolo omgwirira ntchito; koma iwowa anali anthu a nkhondo, akazembe ake aakulu, ndi akulu a magaleta ake, ndi apakavalo ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma mwa ana a Israele Solomoni sanawayese akapolo omgwirira ntchito; koma iwowa anali anthu a nkhondo, akazembe ake akulu, ndi akulu a magaleta ake, ndi apakavalo ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma Aisraele Solomoni sankaŵagwiritsa ntchito yaukapolo. Iwowo anali anthu ake ankhondo, nduna zake, oyang'anira magaleta ake ndi anthu ake okwera pa akavalo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma Solomoni sanagwiritse ntchito ya ukapolo Aisraeli; Iwo anali anthu ake ankhondo, atsogoleri a ankhondo, olamulira magaleta ndi oyendetsa magaleta ake. Onani mutuwo |