2 Mbiri 8:8 - Buku Lopatulika8 mwa ana ao otsala m'dziko pambuyo pao, amene ana a Israele sanawathe, mwa iwowa Solomoni anawachititsa thangata mpaka lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 mwa ana ao otsala m'dziko pambuyo pao, amene ana a Israele sanawathe, mwa iwowa Solomoni anawachititsa thangata mpaka lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 ndiye kuti zidzukulu zao zidaatsalira m'dzikomo, Aisraele ataloŵamo. Onsewo Aisraele sadaŵaononge. Anthu ameneŵa Solomoni ankaŵagwiritsa ntchito yathangata. Ndipo akugwirabe ntchito imeneyo mpaka lero lino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Zimenezi ndiye zinali zidzukulu zawo zotsalira mʼdzikoli, anthu amene Aisraeli sanathe kuwawononga kotheratu. Solomoni anawatenga ndi kukhala akapolo ake ogwira ntchito yathangata, monga zilili mpaka lero lino. Onani mutuwo |