Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 8:10 - Buku Lopatulika

10 Amenewa anali akulu a akapitao a mfumu Solomoni, ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu akulamulira anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Amenewa anali akulu a akapitao a mfumu Solomoni, ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu akulamulira anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ndipo akuluakulu a mfumu Solomoni analipo 250 amene ankalamulira anthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Amenewa ndiwo anali akuluakulu oyangʼanira ntchito za mfumu Solomoni. Onse amene ankayangʼanira anthu analipo 250.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 8:10
5 Mawu Ofanana  

osawerenga akapitao a Solomoni akuyang'anira ntchito, ndiwo zikwi zitatu mphambu mazana atatu, amenewo analamulira anthu aja akugwira ntchito.


Amenewo anali akulu a akapitao oyang'anira ntchito ya Solomoni, mazana asanu mphambu makumi asanu akulamulira anthu ogwira ntchito aja.


Ndipo anaika zikwi makumi asanu ndi awiri za iwowa asenze mirimo, ndi zikwi makumi asanu ndi atatu ateme m'mapiri, ndi akapitao zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi agwiritse anthu ntchito.


Ndipo Solomoni anamkweretsa mwana wamkazi wa Farao m'mzinda wa Davide, alowe m'nyumba imene adammangira; pakuti anati, Mkazi wanga asakhale m'nyumba ya Davide mfumu ya Israele; popeza mpopatulika pamene panafika likasa la Yehova.


Koma mwa ana a Israele Solomoni sanawayese akapolo omgwirira ntchito; koma iwowa anali anthu a nkhondo, akazembe ake aakulu, ndi akulu a magaleta ake, ndi apakavalo ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa