2 Mbiri 7:4 - Buku Lopatulika4 Pamenepo mfumu ndi anthu onse anapereka nsembe pamaso pa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pamenepo mfumu ndi anthu onse anapereka nsembe pamaso pa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono mfumu pamodzi ndi anthu onsewo adapereka nsembe pamaso pa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tsono mfumu ndi anthu onse anapereka nsembe pamaso pa Yehova. Onani mutuwo |